Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 13:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero Mulungu anachititsa ana a Isiraeli kuyenda njira yaitali yodutsa m’chipululu chapafupi ndi Nyanja Yofiira.+ Koma iwo potuluka m’dziko la Iguputo, anayenda mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+

  • Numeri 32:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma atumiki anufe tiwoloka, aliyense atakonzekera kukamenya nkhondo+ pamaso pa Yehova, monga mwanenera mbuyathu.”

  • Yoswa 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Akazi anu ndi ana anu aang’ono atsale limodzi ndi ziweto zanu m’dziko lino limene Mose anakupatsani, tsidya lino la Yorodano.+ Koma amunanu, mudzawoloka patsogolo pa abale anu, mutafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+ Inuyo, amuna nonse amphamvu ndi olimba mtima,+ muwoloke kuti mukawathandize abale anu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena