Ekisodo 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero Mulungu anachititsa ana a Isiraeli kuyenda njira yaitali yodutsa m’chipululu chapafupi ndi Nyanja Yofiira.+ Koma iwo potuluka m’dziko la Iguputo, anayenda mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+ Numeri 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aliyense wokonzekera nkhondo awoloke Yorodano pamaso pa Yehova, kufikira iye atapitikitsa adani ake pamaso pake,+ Deuteronomo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chotero ndinakulamulani pa nthawi imeneyo kuti, ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna nonse olimba mtima muwoloke, mukuyenda patsogolo pa abale anu, ana a Isiraeli, muli okonzeka ndi zida.+
18 Chotero Mulungu anachititsa ana a Isiraeli kuyenda njira yaitali yodutsa m’chipululu chapafupi ndi Nyanja Yofiira.+ Koma iwo potuluka m’dziko la Iguputo, anayenda mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+
21 Aliyense wokonzekera nkhondo awoloke Yorodano pamaso pa Yehova, kufikira iye atapitikitsa adani ake pamaso pake,+
18 “Chotero ndinakulamulani pa nthawi imeneyo kuti, ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna nonse olimba mtima muwoloke, mukuyenda patsogolo pa abale anu, ana a Isiraeli, muli okonzeka ndi zida.+