Yoswa 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anatsetserekera kumadzulo kumalire a Ayafeleti, mpaka kukafika kumalire a Beti-horoni Wakumunsi+ ndi Gezeri,+ n’kukathera kunyanja.+ 1 Mafumu 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Solomo anamanganso Gezeri, Beti-horoni Wakumunsi,+
3 Kenako anatsetserekera kumadzulo kumalire a Ayafeleti, mpaka kukafika kumalire a Beti-horoni Wakumunsi+ ndi Gezeri,+ n’kukathera kunyanja.+