Ekisodo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi mpweya wotuluka m’mphuno mwanu,+ madzi anaunjikika pamodzi.Madzi oyenda anaima ngati khoma.Madzi amphamvu anaundana pakatikati pa nyanja. Salimo 114:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyanja inaona ndipo inathawa.+Yorodano anabwerera m’mbuyo.+
8 Ndi mpweya wotuluka m’mphuno mwanu,+ madzi anaunjikika pamodzi.Madzi oyenda anaima ngati khoma.Madzi amphamvu anaundana pakatikati pa nyanja.