Yoswa 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 n’kukathera kunyanja. Kumpoto kwake kunali Mikametatu,+ ndipo malirewo anazungulira chakum’mawa kukafika ku Taanatu-silo, n’kupitirirabe chakum’mawa mpaka ku Yanoa.
6 n’kukathera kunyanja. Kumpoto kwake kunali Mikametatu,+ ndipo malirewo anazungulira chakum’mawa kukafika ku Taanatu-silo, n’kupitirirabe chakum’mawa mpaka ku Yanoa.