Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 48:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma bambo akewo anakanabe, kuti: “Ndikudziwa mwana wanga, ndikudziwa zimenezo. Uyunso adzakhala mtundu wa anthu, ndipo adzakhala wamkulu.+ Koma mng’ono wakeyu adzakhala wamkulu kuposa iyeyu,+ ndipo mbadwa zake zidzachuluka kwambiri n’kupanga mitundu ya anthu.”+

  • Numeri 26:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Amenewa ndiwo anali mabanja a Manase. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 52,700.+

  • Numeri 26:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Amenewa ndiwo anali mabanja a ana a Efuraimu.+ Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 32,500. Awa anali ana aamuna a Yosefe ndi mabanja awo.+

  • Deuteronomo 33:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ulemerero wake ndi wofanana ndi wa mwana wa ng’ombe wamphongo woyamba kubadwa,+

      Ndipo nyanga zake ndi nyanga za ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+

      Nyanga zimenezo adzakankha nazo anthu.+

      Adzakankha nazo anthu onse pamodzi mpaka kukafika kumalekezero a dziko lapansi.

      Nyanga zimenezo ndi anthu masauzande makumimakumi a fuko la Efuraimu,+

      Ndiponso anthu masauzande a fuko la Manase.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena