Yoswa 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kuchokera m’fuko la Isakara,+ anawapatsa Kisioni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Daberati+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 1 Mbiri 6:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Kuchokera ku fuko la Isakara, anawapatsa mzinda wa Kedesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Daberati+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
28 Kuchokera m’fuko la Isakara,+ anawapatsa Kisioni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Daberati+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
72 Kuchokera ku fuko la Isakara, anawapatsa mzinda wa Kedesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Daberati+ ndi malo ake odyetserako ziweto,