Yoswa 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako malirewo anakhota n’kubwerera kulowera kum’mawa kwa Saridi mpaka kumalire a Kisilotu-tabori. Ndiyeno anapitirira kukafika ku Daberati+ mpaka ku Yafiya.
12 Kenako malirewo anakhota n’kubwerera kulowera kum’mawa kwa Saridi mpaka kumalire a Kisilotu-tabori. Ndiyeno anapitirira kukafika ku Daberati+ mpaka ku Yafiya.