Yoswa 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho amuna opita kukalemba dzikowo ananyamuka kuti azipita, ndipo Yoswa anawalamula+ kuti: “Pitani mukayendere dzikolo n’kulemba mmene lilili. Mukatero mubwerere kwa ine, ndipo ineyo ndidzakuchitirani maere+ pamaso pa Yehova kuno ku Silo.”+
8 Choncho amuna opita kukalemba dzikowo ananyamuka kuti azipita, ndipo Yoswa anawalamula+ kuti: “Pitani mukayendere dzikolo n’kulemba mmene lilili. Mukatero mubwerere kwa ine, ndipo ineyo ndidzakuchitirani maere+ pamaso pa Yehova kuno ku Silo.”+