Numeri 35:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kwa ana a Isiraeli, kwa mlendo,+ ndi kwa munthu amene wakhaliratu pakati pawo, mizinda 6 imeneyi ikakhala kothawirako aliyense amene wapha munthu mwangozi.+
15 Kwa ana a Isiraeli, kwa mlendo,+ ndi kwa munthu amene wakhaliratu pakati pawo, mizinda 6 imeneyi ikakhala kothawirako aliyense amene wapha munthu mwangozi.+