Numeri 35:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mizinda 6 imeneyi ikakhale kothawirako Aisiraeli, mlendo+ komanso munthu aliyense amene akukhala pakati pawo, aliyense amene wapha munthu mwangozi.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:15 Nsanja ya Olonda,11/15/1995, ptsa. 10-14, 16-17
15 Mizinda 6 imeneyi ikakhale kothawirako Aisiraeli, mlendo+ komanso munthu aliyense amene akukhala pakati pawo, aliyense amene wapha munthu mwangozi.+