Numeri 35:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kwa ana a Isiraeli, kwa mlendo,+ ndi kwa munthu amene wakhaliratu pakati pawo, mizinda 6 imeneyi ikakhala kothawirako aliyense amene wapha munthu mwangozi.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:15 Nsanja ya Olonda,11/15/1995, ptsa. 10-14, 16-17
15 Kwa ana a Isiraeli, kwa mlendo,+ ndi kwa munthu amene wakhaliratu pakati pawo, mizinda 6 imeneyi ikakhala kothawirako aliyense amene wapha munthu mwangozi.+