Yoswa 20:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Sankhani mizinda yothawirako+ imene ndinakuuzani kudzera mwa Mose, 3 kuti wopha munthu mwangozi* azithawirako pothawa wobwezera magazi.+
2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Sankhani mizinda yothawirako+ imene ndinakuuzani kudzera mwa Mose, 3 kuti wopha munthu mwangozi* azithawirako pothawa wobwezera magazi.+