-
Numeri 35:14, 15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yorodano,+ ndiponso mukapereke mizinda itatu tsidya linalo, mʼdziko la Kanani.+ Imeneyi ikakhala mizinda yothawirako. 15 Mizinda 6 imeneyi ikakhale kothawirako Aisiraeli, mlendo+ komanso munthu aliyense amene akukhala pakati pawo, aliyense amene wapha munthu mwangozi.+
-