-
Deuteronomo 19:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Yehova Mulungu wanu akadzawonjezera dziko lanu mogwirizana ndi zimene analumbira kwa makolo anu,+ nʼkukupatsani dziko lonse limene analonjeza makolo anu kuti adzawapatsa,+ 9 (ngati mutatsatira mokhulupirika malamulo onsewa amene ndikukupatsani lero, akuti muzikonda Yehova Mulungu wanu komanso kuyenda mʼnjira zake nthawi zonse+) mudzawonjezere mizinda inanso itatu pa mizinda imeneyi.+
-