Oweruza 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mukakafika kumeneko, mukapeza anthu okhala mosatekeseka,+ ndipo dzikolo ndi lalikulu kwambiri. Mulungu walipereka m’manja mwanu,+ ndipo ndi dziko losasowa kena kalikonse kopezeka padziko lapansi.”+
10 Mukakafika kumeneko, mukapeza anthu okhala mosatekeseka,+ ndipo dzikolo ndi lalikulu kwambiri. Mulungu walipereka m’manja mwanu,+ ndipo ndi dziko losasowa kena kalikonse kopezeka padziko lapansi.”+