Oweruza 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno apongozi akewo, bambo a mtsikanayo, anam’chonderera kuti akhalebe, moti anakhala ndi kugona kumeneko masiku atatu. Masiku onsewa, iwo anali kudya ndi kumwa.+ 1 Petulo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muzicherezana popanda kudandaula.+
4 Ndiyeno apongozi akewo, bambo a mtsikanayo, anam’chonderera kuti akhalebe, moti anakhala ndi kugona kumeneko masiku atatu. Masiku onsewa, iwo anali kudya ndi kumwa.+