Oweruza 20:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma amuna 600 anatembenuka ndi kuthawira kuchipululu kuthanthwe la Rimoni. Iwo anapitiriza kukhala kuthanthwe la Rimoni+ kwa miyezi inayi. Oweruza 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno khamu lonse linatumiza anthu kukalankhula ndi ana a Benjamini amene anali kukhala kuthanthwe la Rimoni,+ ndi kuwalonjeza mtendere.
47 Koma amuna 600 anatembenuka ndi kuthawira kuchipululu kuthanthwe la Rimoni. Iwo anapitiriza kukhala kuthanthwe la Rimoni+ kwa miyezi inayi.
13 Ndiyeno khamu lonse linatumiza anthu kukalankhula ndi ana a Benjamini amene anali kukhala kuthanthwe la Rimoni,+ ndi kuwalonjeza mtendere.