Oweruza 20:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Chotero anatembenuka ndi kuthawira kuchipululu, kuthanthwe la Rimoni.+ Aisiraeli anapululanso ana a Benjamini 5,000 m’misewu ikuluikulu,+ ndipo anapitiriza kuwathamangitsa mpaka kukafika ku Gidomu ndi kuphanso amuna ena 2,000. Oweruza 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno khamu lonse linatumiza anthu kukalankhula ndi ana a Benjamini amene anali kukhala kuthanthwe la Rimoni,+ ndi kuwalonjeza mtendere.
45 Chotero anatembenuka ndi kuthawira kuchipululu, kuthanthwe la Rimoni.+ Aisiraeli anapululanso ana a Benjamini 5,000 m’misewu ikuluikulu,+ ndipo anapitiriza kuwathamangitsa mpaka kukafika ku Gidomu ndi kuphanso amuna ena 2,000.
13 Ndiyeno khamu lonse linatumiza anthu kukalankhula ndi ana a Benjamini amene anali kukhala kuthanthwe la Rimoni,+ ndi kuwalonjeza mtendere.