Oweruza 20:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma amuna 600 anatembenuka ndi kuthawira kuchipululu kuthanthwe la Rimoni. Iwo anapitiriza kukhala kuthanthwe la Rimoni+ kwa miyezi inayi.
47 Koma amuna 600 anatembenuka ndi kuthawira kuchipululu kuthanthwe la Rimoni. Iwo anapitiriza kukhala kuthanthwe la Rimoni+ kwa miyezi inayi.