Numeri 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano mfumu ya Akanani ya ku Aradi+ yomwe inali kukhala ku Negebu,+ inamva kuti Aisiraeli akubwera kudzera njira ya ku Atarimu. Itamva zimenezo inapita kukamenyana nawo ndipo Aisiraeli ena inawagwira ndi kupita nawo kudziko lake.
21 Tsopano mfumu ya Akanani ya ku Aradi+ yomwe inali kukhala ku Negebu,+ inamva kuti Aisiraeli akubwera kudzera njira ya ku Atarimu. Itamva zimenezo inapita kukamenyana nawo ndipo Aisiraeli ena inawagwira ndi kupita nawo kudziko lake.