Oweruza 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu onse a m’badwo umenewo anamwalira ndi kugona ndi makolo awo,+ ndipo pambuyo pawo panauka m’badwo wina umene sunadziwe Yehova kapena ntchito zimene iye anachitira Isiraeli.+
10 Anthu onse a m’badwo umenewo anamwalira ndi kugona ndi makolo awo,+ ndipo pambuyo pawo panauka m’badwo wina umene sunadziwe Yehova kapena ntchito zimene iye anachitira Isiraeli.+