Oweruza 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo anthuwo anapitiriza kutumikira Yehova masiku onse a Yoswa ndi masiku onse a akulu amene anapitiriza kukhala ndi moyo Yoswa atamwalira, akulu amene anaona ntchito zonse zazikulu zimene Yehova anachitira Isiraeli.+ Mlaliki 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’badwo umapita+ ndipo m’badwo wina umabwera,+ koma dziko lapansi lidzakhalapobe mpaka kalekale.*+
7 Ndipo anthuwo anapitiriza kutumikira Yehova masiku onse a Yoswa ndi masiku onse a akulu amene anapitiriza kukhala ndi moyo Yoswa atamwalira, akulu amene anaona ntchito zonse zazikulu zimene Yehova anachitira Isiraeli.+