Oweruza 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ehudi atamwalira, ana a Isiraeli anayambanso kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+