Yoswa 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atachoka kumeneko anapita kukamenyana ndi anthu a ku Debiri.+ (Zimenezi zisanachitike, Debiri ankatchedwa Kiriyati-seferi.)+
15 Atachoka kumeneko anapita kukamenyana ndi anthu a ku Debiri.+ (Zimenezi zisanachitike, Debiri ankatchedwa Kiriyati-seferi.)+