-
Yoswa 10:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Analanda mzindawo ndi midzi yake yonse n’kugwiranso mfumu yake. Ndiyeno anapha ndi lupanga munthu aliyense amene anali mmenemo,+ ndipo Yoswa anaonetsetsa kuti pasakhale wopulumuka.+ Anachitira mzinda wa Debiri ndi mfumu yake zonse zimene anachitira mzinda wa Heburoni, komanso zimene anachitira mzinda wa Libina ndi mfumu yake.+
-