Salimo 105:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muimbireni, muimbireni nyimbo zomutamanda,+Sinkhasinkhani ntchito zake zonse zodabwitsa.+ Salimo 145:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzasinkhasinkha za ulemerero wanu waukulu+Ndi nkhani zokhudza ntchito zanu zodabwitsa.+