Numeri 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anamva mawu a Aisiraeli, ndipo anapereka Akananiwo m’manja mwawo. Aisiraeli anawononga Akananiwo limodzi ndi mizinda yawo. N’chifukwa chake malowo anawatcha Horima.*+ Yoswa 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Elitoladi,+ Betuli, Horima, 1 Mbiri 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ku Betuele,+ ku Horima,+ ku Zikilaga,+
3 Yehova anamva mawu a Aisiraeli, ndipo anapereka Akananiwo m’manja mwawo. Aisiraeli anawononga Akananiwo limodzi ndi mizinda yawo. N’chifukwa chake malowo anawatcha Horima.*+