Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pambuyo pake, mngelo wa Yehova+ anakapeza Hagara m’chipululu ali pakasupe wamadzi wa panjira yopita ku Shura.+

  • Genesis 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno Hagara anayamba kutchula dzina la Yehova n’kunena kuti: “Inu ndinu Mulungu amene amaona chilichonse.”*+ Anatinso: “Kodi nanenso pano ndaona wotha kundionayo?”

  • Genesis 32:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Potsirizira pake, Yakobo anatsala yekhayekha. Kenako, munthu winawake anayamba kulimbana naye usiku wonse mpaka m’bandakucha.+

  • Genesis 32:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Chotero Yakobo anatcha malowo Penieli,*+ chifukwa iye anati, “Ndaonana ndi Mulungu pamasom’pamaso, komabe ndapulumuka.”+

  • Oweruza 13:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno Manowa anauza mkazi wake kuti: “Ife tifa basi,+ chifukwa taona Mulungu.”+

  • Luka 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano Zekariya anavutika mumtima ataona zimenezo, ndipo anagwidwa ndi mantha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena