Oweruza 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Gidiyoni anazindikira kuti anali mngelo wa Yehova.+ Nthawi yomweyo Gidiyoni anati: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Ndaonana ndi mngelo wa Yehova maso ndi maso.”+ Danieli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ndinatsala ndekha ndipo ndinaona masomphenya odabwitsawa. Pamenepo mphamvu zonse zinandithera, ndipo maonekedwe olemekezeka a nkhope yanga anasintha kwambiri n’kukhala omvetsa chisoni, moti ndinalibenso mphamvu.+ Machitidwe 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Koneliyo anayang’anitsitsa mngelo uja, ndipo mantha atamugwira anati: “N’chiyani Mbuyanga?” Mngeloyo anamuuza kuti: “Mapemphero ako+ ndi mphatso zako zachifundo zakwera kwa Mulungu monga chikumbutso.+ Chivumbulutso 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nditamuona, ndinagwa pamapazi ake ngati kuti ndafa. Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja ndi kundiuza kuti: “Usachite mantha.+ Ine ndine Woyamba+ ndi Wotsiriza,+
22 Tsopano Gidiyoni anazindikira kuti anali mngelo wa Yehova.+ Nthawi yomweyo Gidiyoni anati: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Ndaonana ndi mngelo wa Yehova maso ndi maso.”+
8 Choncho ndinatsala ndekha ndipo ndinaona masomphenya odabwitsawa. Pamenepo mphamvu zonse zinandithera, ndipo maonekedwe olemekezeka a nkhope yanga anasintha kwambiri n’kukhala omvetsa chisoni, moti ndinalibenso mphamvu.+
4 Pamenepo Koneliyo anayang’anitsitsa mngelo uja, ndipo mantha atamugwira anati: “N’chiyani Mbuyanga?” Mngeloyo anamuuza kuti: “Mapemphero ako+ ndi mphatso zako zachifundo zakwera kwa Mulungu monga chikumbutso.+
17 Nditamuona, ndinagwa pamapazi ake ngati kuti ndafa. Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja ndi kundiuza kuti: “Usachite mantha.+ Ine ndine Woyamba+ ndi Wotsiriza,+