Genesis 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero Abulahamu anatcha malowo Yehova-yire.* Ndiye chifukwa chake lero pali mawu akuti: “M’phiri lake Yehova adzapereka zinthu zofunikira.”+ Ekisodo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Mose anamanga guwa lansembe n’kulitcha kuti Yehova-nisi,*
14 Chotero Abulahamu anatcha malowo Yehova-yire.* Ndiye chifukwa chake lero pali mawu akuti: “M’phiri lake Yehova adzapereka zinthu zofunikira.”+