Genesis 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Elifazi mwana wa Esau anali ndi mdzakazi dzina lake Timina.+ Patapita nthawi, mdzakaziyu anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Amenewa ndiwo anali ana a Ada mkazi wa Esau. Ekisodo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ndipo anati: “Popeza dzanja laukira mpando wachifumu+ wa Ya,+ Yehova adzamenya nkhondo ndi Aamaleki ku mibadwomibadwo.”+ Numeri 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Balamu ataona Amaleki, anapitiriza mawu ake a ndakatulo, kuti:+“Amaleki anali woyamba wa anthu a mitundu ina,+Koma chiwonongeko chake chidzakhaladi mapeto ake.”+ Deuteronomo 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi.
12 Elifazi mwana wa Esau anali ndi mdzakazi dzina lake Timina.+ Patapita nthawi, mdzakaziyu anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Amenewa ndiwo anali ana a Ada mkazi wa Esau.
16 ndipo anati: “Popeza dzanja laukira mpando wachifumu+ wa Ya,+ Yehova adzamenya nkhondo ndi Aamaleki ku mibadwomibadwo.”+
20 Tsopano Balamu ataona Amaleki, anapitiriza mawu ake a ndakatulo, kuti:+“Amaleki anali woyamba wa anthu a mitundu ina,+Koma chiwonongeko chake chidzakhaladi mapeto ake.”+
19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi.