Oweruza 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana a Isiraeli anakhala pakati pa Akanani,+ amene ndi Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+