Oweruza 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Fuko la Efuraimu nalonso silinapitikitse Akanani amene anali kukhala ku Gezeri, moti Akananiwo anakhalabe pakati pawo ku Gezeriko.+ Salimo 106:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwowa sanawononge mitundu ina ya anthu,+Mmene Yehova anawauzira.+
29 Fuko la Efuraimu nalonso silinapitikitse Akanani amene anali kukhala ku Gezeri, moti Akananiwo anakhalabe pakati pawo ku Gezeriko.+