Yoswa 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+ 1 Mafumu 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 (M’mbuyomo, Farao mfumu ya Iguputo inabwera n’kulanda mzinda wa Gezeri n’kuutentha ndi moto. Akanani+ okhala mumzindawo inawapha. Kenako inaupereka kwa mwana wake wamkazi+ monga mphatso pamene anali kukwatiwa ndi Solomo.)
10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+
16 (M’mbuyomo, Farao mfumu ya Iguputo inabwera n’kulanda mzinda wa Gezeri n’kuutentha ndi moto. Akanani+ okhala mumzindawo inawapha. Kenako inaupereka kwa mwana wake wamkazi+ monga mphatso pamene anali kukwatiwa ndi Solomo.)