Oweruza 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi Mulungu sanapereke Orebi ndi Zeebi,+ akalonga a Midiyani m’manja mwanu? Ndipo ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?” Atanena mawu amenewa, mkwiyo wawo unaphwa.+ Salimo 83:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atsogoleri awo muwachititse kukhala ngati Orebi ndi Zeebi.+Ndipo mafumu awo onse muwachititse kukhala ngati Zeba ndi Zalimuna.+
3 Kodi Mulungu sanapereke Orebi ndi Zeebi,+ akalonga a Midiyani m’manja mwanu? Ndipo ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?” Atanena mawu amenewa, mkwiyo wawo unaphwa.+
11 Atsogoleri awo muwachititse kukhala ngati Orebi ndi Zeebi.+Ndipo mafumu awo onse muwachititse kukhala ngati Zeba ndi Zalimuna.+