Oweruza 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anapereka Orebi ndi Zeebi,+ akalonga a Midiyani mʼmanja mwanu. Ndiye ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?” Atanena mawu amenewa, mkwiyo wawo unatha. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Nsanja ya Olonda,8/15/2000, tsa. 25
3 Mulungu anapereka Orebi ndi Zeebi,+ akalonga a Midiyani mʼmanja mwanu. Ndiye ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?” Atanena mawu amenewa, mkwiyo wawo unatha.