Oweruza 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi Mulungu sanapereke Orebi ndi Zeebi,+ akalonga a Midiyani m’manja mwanu? Ndipo ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?” Atanena mawu amenewa, mkwiyo wawo unaphwa.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Nsanja ya Olonda,8/15/2000, tsa. 25
3 Kodi Mulungu sanapereke Orebi ndi Zeebi,+ akalonga a Midiyani m’manja mwanu? Ndipo ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?” Atanena mawu amenewa, mkwiyo wawo unaphwa.+