Oweruza 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Gidiyoni anawauza kuti: “N’chifukwa chake Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna m’manja mwanga, ndithu, ndidzakukwapulani ndi mitengo yaminga ya m’chipululu komanso ndi zitsamba zaminga.”+ Miyambo 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamilomo ya munthu womvetsa zinthu pamapezeka nzeru,+ koma ndodo amakwapulira msana wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+ Miyambo 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zilango anazikhazikitsira anthu onyoza,+ ndipo zikwapu anazisungira msana wa anthu opusa.+
7 Pamenepo Gidiyoni anawauza kuti: “N’chifukwa chake Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna m’manja mwanga, ndithu, ndidzakukwapulani ndi mitengo yaminga ya m’chipululu komanso ndi zitsamba zaminga.”+
13 Pamilomo ya munthu womvetsa zinthu pamapezeka nzeru,+ koma ndodo amakwapulira msana wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+