Oweruza 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Zeba ndi Zalimuna anati: “Nyamuka iweyo utiphe wekha. Munthu amakhala ndi mphamvu+ zolingana ndi msinkhu wake.” Motero Gidiyoni ananyamuka ndi kupha+ Zeba ndi Zalimuna, ndipo anatenga zokongoletsa zooneka ngati mwezi zimene zinali pakhosi la ngamila zawo. Yesaya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’tsiku limenelo Yehova adzachotsa zokongoletsera zawo zonse: zibangili za m’miyendo, zinthu zomanga kumutu, zodzikongoletsera zooneka ngati mwezi,+
21 Choncho Zeba ndi Zalimuna anati: “Nyamuka iweyo utiphe wekha. Munthu amakhala ndi mphamvu+ zolingana ndi msinkhu wake.” Motero Gidiyoni ananyamuka ndi kupha+ Zeba ndi Zalimuna, ndipo anatenga zokongoletsa zooneka ngati mwezi zimene zinali pakhosi la ngamila zawo.
18 M’tsiku limenelo Yehova adzachotsa zokongoletsera zawo zonse: zibangili za m’miyendo, zinthu zomanga kumutu, zodzikongoletsera zooneka ngati mwezi,+