1 Samueli 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+ Salimo 83:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atsogoleri awo muwachititse kukhala ngati Orebi ndi Zeebi.+Ndipo mafumu awo onse muwachititse kukhala ngati Zeba ndi Zalimuna.+
33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+
11 Atsogoleri awo muwachititse kukhala ngati Orebi ndi Zeebi.+Ndipo mafumu awo onse muwachititse kukhala ngati Zeba ndi Zalimuna.+