Oweruza 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Tsopano kodi mwachita zimenezi m’choonadi komanso kuchokera pansi pa mtima, moti mwalonga Abimeleki ufumu?+ Ndipo kodi Yerubaala ndi nyumba yake mwamuchitira zinthu zabwino? Kodi mwamuchitira mogwirizana ndi zimene iye anachita, Mlaliki 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mumzindawo munali munthu wina wosauka koma wanzeru, amene anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zake.+ Koma kenako palibe amene anakumbukira munthu wosaukayo.+ 2 Timoteyo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti anthu adzakhala odzikonda, okonda ndalama, odzimva, odzikweza, onyoza, osamvera makolo,+ osayamika, osakhulupirika,+
16 “Tsopano kodi mwachita zimenezi m’choonadi komanso kuchokera pansi pa mtima, moti mwalonga Abimeleki ufumu?+ Ndipo kodi Yerubaala ndi nyumba yake mwamuchitira zinthu zabwino? Kodi mwamuchitira mogwirizana ndi zimene iye anachita,
15 Mumzindawo munali munthu wina wosauka koma wanzeru, amene anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zake.+ Koma kenako palibe amene anakumbukira munthu wosaukayo.+
2 Pakuti anthu adzakhala odzikonda, okonda ndalama, odzimva, odzikweza, onyoza, osamvera makolo,+ osayamika, osakhulupirika,+