2 Samueli 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abisalomu anapitiriza kuchita zinthu zoterezi kwa Aisiraeli onse amene anali kubwera kwa mfumu kuti iwaweruzire milandu yawo, moti Abisalomu anapitiriza kukopa mitima ya anthu a mu Isiraeli.+
6 Abisalomu anapitiriza kuchita zinthu zoterezi kwa Aisiraeli onse amene anali kubwera kwa mfumu kuti iwaweruzire milandu yawo, moti Abisalomu anapitiriza kukopa mitima ya anthu a mu Isiraeli.+