Miyambo 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuli bwino kukhala wodzichepetsa limodzi ndi anthu ofatsa,+ kusiyana n’kugawana katundu wolanda ndi anthu odzikuza.+
19 Kuli bwino kukhala wodzichepetsa limodzi ndi anthu ofatsa,+ kusiyana n’kugawana katundu wolanda ndi anthu odzikuza.+