Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mapeto a chinthu amakhala bwino kuposa chiyambi chake,+ ndipo munthu woleza mtima ndi wabwino kuposa munthu wodzikuza.+

  • Yesaya 57:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti Wapamwamba ndi Wokwezeka,+ yemwe adzakhalepo kwamuyaya+ ndiponso yemwe dzina lake ndi loyera,+ wanena kuti: “Ine ndimakhala kumwamba pamalo oyera.+ Ndimakhalanso ndi munthu wopsinjika ndi wa mtima wodzichepetsa,+ kuti nditsitsimutse mtima wa anthu onyozeka ndiponso kuti nditsitsimutse mtima wa anthu opsinjika.+

  • Yeremiya 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Koma amene akudzitamanda adzitamande pa chifukwa chakuti, amamvetsa bwino+ njira zanga ndipo amandidziwa, kuti ine ndine Yehova,+ amene ndimasonyeza kukoma mtima kosatha, ndimapereka ziweruzo ndi kuchita chilungamo padziko lapansi.+ Pakuti zinthu zimenezi zimandisangalatsa,”+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena