1 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi? Salimo 115:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Mulungu wathu ali kumwamba.+Chilichonse chimene anafuna kuchita anachita.+
27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi?