Salimo 138:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti Yehova ali pamwamba, amaona wodzichepetsa,+Koma wodzikuza samuyandikira.+ Miyambo 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa cha kudzikuza, munthu amangoyambitsa mavuto,+ koma anthu amene amakhala pamodzi n’kumakambirana amakhala ndi nzeru.+ Agalatiya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ngati wina akudziona kuti ndi wofunika pamene si wotero,+ akudzinyenga. Yakobo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Abale, pa nkhani ya kumva zowawa+ ndi kuleza mtima,+ tengerani chitsanzo+ kwa aneneri+ amene analankhula m’dzina la Yehova.+ 1 Petulo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+
10 Chifukwa cha kudzikuza, munthu amangoyambitsa mavuto,+ koma anthu amene amakhala pamodzi n’kumakambirana amakhala ndi nzeru.+
10 Abale, pa nkhani ya kumva zowawa+ ndi kuleza mtima,+ tengerani chitsanzo+ kwa aneneri+ amene analankhula m’dzina la Yehova.+
5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+