Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 8:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pamenepo amuna a ku Efuraimu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenya nkhondo ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anayesetsa mwamphamvu kuti achite naye mkangano.+

  • Oweruza 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno amuna a ku Efuraimu anasonkhana pamodzi n’kuwolokera tsidya lina chakumpoto, ndi kuuza Yefita kuti: “N’chifukwa chiyani unawoloka kukamenya ndi ana a Amoni ife osatiitana kuti tipite nawe?+ Tikutentha ndi moto pamodzi ndi nyumba yako.”+

  • Miyambo 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+

  • Miyambo 21:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Munthu amene amadzikuza akapsa mtima, amatchedwa wodzikuza, wonyada ndi wodzitama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena