Oweruza 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Anthu amene uli nawowa ndi ochuluka kwambiri kuti ndipereke Amidiyani m’manja mwawo,+ chifukwa mwina Isiraeli angadzitukumule+ pamaso panga ndi kunena kuti, ‘Ndinadzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.’+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+ Miyambo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kunyada kumafikitsa munthu ku chiwonongeko,+ ndipo mtima wodzikuza umachititsa munthu kupunthwa.+
2 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Anthu amene uli nawowa ndi ochuluka kwambiri kuti ndipereke Amidiyani m’manja mwawo,+ chifukwa mwina Isiraeli angadzitukumule+ pamaso panga ndi kunena kuti, ‘Ndinadzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.’+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+