Oweruza 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo amuna a ku Efuraimu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenya nkhondo ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anayesetsa mwamphamvu kuti achite naye mkangano.+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+ Miyambo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kunyada kumafikitsa munthu ku chiwonongeko,+ ndipo mtima wodzikuza umachititsa munthu kupunthwa.+ Yakobo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti pamene pali nsanje+ ndi mtima wokonda mikangano, palinso chisokonezo ndi zoipa zamtundu uliwonse.+
8 Pamenepo amuna a ku Efuraimu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenya nkhondo ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anayesetsa mwamphamvu kuti achite naye mkangano.+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+
16 Pakuti pamene pali nsanje+ ndi mtima wokonda mikangano, palinso chisokonezo ndi zoipa zamtundu uliwonse.+